Skip to main content

CHIPANI CHATSOPANO CHA MDP CHATI CHIZAPAMBANA PACHISANKHO

Mtsogoleri wa Chipani chatsopano mdziko muno Cha Malawian Dream Party (MDP) Musa Zalira wauza nyumba zofalitsa nkhani kuti chidzapambana pachisankho cha chaka chino.

Iye wati chipani chawo chibwerenzetsa chikhulupiliro Cha anthu ambiri maka achinyanata.

Chipani cha MDP chati chilembetsa mu kaundula wa zipani mwezi uno usanathe ndipo chipanga mgwirizano ndi zipani zokhazo zimene zikuyika achimata patsogolo.

Katswiri pa nkhani za ndale wonderful Mkhuche wati akukaika ngati chipanichi chikhale ndi nthawi yozigulitsila poti kwangotsala miyezi isanu ndi iwiri (7) kuti dziko lino lichititae chisankho mu mwezi wa Seputambala pa 16.

Masiku apitawa guru lina linayambiysanso chipani china Cha National Youth Alliance ndipo akuti ndi cha achinyanata.


(Daire Media Group)

Comments

Popular posts from this blog

MALUBA ALBUM RELEASE

The Mzuzu based afro artist Merchah is set to release his first ever album titled "Maluba" on 30th January 2025 Before this new release the Afro Star whose real name is Uchizi Msowoya has produced other new songs which were released in 2024 in which he had featured among other renowned local artists Namadingo and Suffix.

MUM SEEKS RECONCILIATION WITH HER REBELLIOUS SONS AFTER YEARS IN HIDING FROM MURDER PLOT

A staged murder that forced mum to escape from her biological sons has finally come on the spotlight after the mother refreshes love and memories for her rebellious children after 19 years in hiding. Picture taken on X The mother whom we have named Mrs Kamanga for security reasons speaks out how she escaped and survived a murder plot by her two biological sons in company of their friends that led the family into a verge of dismantling the bond that existed between mother and children. No one knew the whereabouts of Mrs Kamanga until the day of this publication when this reporter bumped into the widow's merchandise after years of hiding in Mzimba when family relations bayed for her blood. She was accused of having a hand into the death of their husband and her daughter. The widow is now running a chain of business merchandise and feels it is time to re-connect and re-unite with her sons. Although she is still scared that her sons may still want her head but she believes that ev...

INTRODUCING OUR FIFTH MEMBER

Mr. Richard Mpezeni (GRAPHICS DESIGNER), Welcome on board🔥🎉