Skip to main content

Posts

Bungwe la Malawi Bureau of Standards (MBS) lero laseka sitolo ya Sana Northern End ili kufupi ndi St Andrews CCAP komaso Sana Wholesale imene ili ku katoto muzinda wa Mzuzu. Izi ndi malingana ndikusatsata ndondomeko za ukhondo musitolozi zomwe zaoneka pomwe bungweli limayendera sitolozi. Mwazina sitolozi zatsekedwa kamba kopezeka ndi zakudya zoonongeka monga nyama, nsomba ndi zina komaso katundu oti masiku ake anatha (expire). Bungwe la MBS lakhala likuyendera sitolo zosiyanasiyana ngat njira imodzi yoonesesa kuti ukhondo ukuyenda bwino.  Izi zikudza pomwe bungweli latsekanso sitolo za Sana ku Blantyre ndi ku Lilongwe pazifukwa zakusowa kwa ukhondo komanso kugulitsa zakudya zoonobgeka zomwe zimapereka chiopsezo chachikulu ku umoyo wa anthu mdziko muno mwa zina. Wolemba Phales Nthambo
Recent posts

TECHNICAL GLITCH PARALYZES DRTSS TRAFFIC SYSTEM, MINISTRY PROMISES SWIFT RESOLUTION

Traffic Information System at the Directorate of Road Traffic and safety Services (DRTSS) has been paralyzed following a technical error encountered at the directorate for over a week. This has negatively impacted the department and its agencies making them unable to provide all the services that are processed through the system. According to the press statement of January 15,2025, from the Ministry of Transport and Public Works the directorate and the system supplier have been struggling to restore the system as expected. "The ministry and the system supplier are working tirelessly to resolve the problem since it was discovered. Despite the urgency to have the system back within the shortest period, the technical nature of the problem required more time to resolve than earlier estimated," said part of the statement signed by secretary for transport and public works Eng.David Mzandu. The ministry has however assured the general public that there is tremendous progress towards...

HAPPY JOHN CHILEMBWE's DAY

 

INTRODUCING OUR SEVENTH MEMBER

Miss. Joyce Gondwe who happens to be our reporter 🎉🔥
 Police in Rumphi have found a dead body of a newborn baby wrapped in a plastic bag and dumped at Matunkha stream in the district. Rumphi Police Spokesperson Noel Kamchenga has confirmed the development saying they suspect it was dumped by unknown woman on Tuesday. They have since launched an investigation to trace and arrest the suspect for infanticide. Trends of dumping newborn babies are on the rise in the country with Nkhatabay alone also registering three consecutive cases in late December last year. Reported by Phales Nthambo - Rumphi

INTRODUCING OUR SIXTH MEMBER

Mr. Alexander Chapola (Broadcaster). Welcome on board🎉🔥🔥
Namondwe wa Dikeledi amene wabuka lachinayi pa nyanja ya mchere ya India akuyembekezeka kufika mdziko la Mozambique la Mulungu lino. Nthambi yowona za nyengo ku Malawi kuno ndi imene yanena izi mu uthenga wake wa lachinayi. Nthambiyi yati pakadali pano palibe zizindikiro zoti Namondweyo atha kufika mdziko muno. By Alice Moyo

INTRODUCING OUR FIFTH MEMBER

Mr. Richard Mpezeni (GRAPHICS DESIGNER), Welcome on board🔥🎉

A CHARLES KACHITSEKO APEZEKA ATAFA

Charles Kachitseko wazaka 33, yemwe wakhala akusowa atadumphila mnyanja ya Malawi kuchokera mu sitima ya MV Ilala lachiwiri usiku wapezeka atafa m'boma la Nkhotakota. Malinga ndi womwe awona izi asodzi ndi amene apeza thupi la mzibamboyo likuyandama. Pakadali pano zotsatila zakupima kwa thupilo pa chipatala cha Nkhotakota zikusonyeza kuti Kachitseko wafa kamba kakubanika. Achibale pamodzi ndi anthu ena ayika kale m'manda thupilo pafupi ndi Dooko la Kaliba m'boma lomwelo. Kachitseko amachokera m'mudzi wa Mwansambo TA Mwansambo ku Nkhotakota komweko ndipo anthu amene anamuwona asanadumphe kuchokera mu sitimayo akuti mkuluyo amamwa mowa mu sitima yomweyo. (Daire Media Group)
Aku likulu la Police mdziko muno ati akusakasaka wa police amene akumuganizira kuti wapha bwenzi lake ku Zomba. Mneneri ku likulu la Polisi Peter kalaya wati Sergeant Peter Chimoyo, anayamba wamenya bwenzi lawolo atasemphana maganizo. Mayiyo anapita ku chipatala cha Domasi kumene wakamwalilira akulandila thandizo la mankhwala. Malimga ndi Kalaya mulandu womwe wapalamula Chimoyo chilango chake ndikukhala ku Ndende moyo wake wonse. Daire Media Group

Devastating Palisade Fire Destroys Thousands of Acres and Forces Mass Evacuations

At least 16,832 Acres have been destroyed and over 30,000 households affected with a continued massive Palisade Fire in the Pacific Palisades Neighborhood. The fire which started on Tuesday 7 January 2025 has since spread quickly due to strong Santa winds with gusts reaching 100 Mph while recording a 0% containment. Mandatory order has been issued to evacuate residents including several areas and parts of Santa Monica and Malibu. Dozens of homes and several schools have been closed as strong winds are making it a challenge for Firefightrers. By Brown Banda

JUDICIAL SERVICE COMMISSION (JSC) RECEIVES 26 CORRUPTION COMPLAINTS

High Court of Malawi Judge Kenan Manda and Magistrate Diana Mangwana are some of the public officers implicated in the 26 corruption complaints that the Judicial Service Commission (JSC) has received. JSC secretary Irene Chikapa said on Wednesday that the former has four counts while the later has eight. Manda is the High Court judge responsible for Commercial Division. (Daire Media Group)

CHIPANI CHATSOPANO CHA MDP CHATI CHIZAPAMBANA PACHISANKHO

Mtsogoleri wa Chipani chatsopano mdziko muno Cha Malawian Dream Party (MDP) Musa Zalira wauza nyumba zofalitsa nkhani kuti chidzapambana pachisankho cha chaka chino. Iye wati chipani chawo chibwerenzetsa chikhulupiliro Cha anthu ambiri maka achinyanata. Chipani cha MDP chati chilembetsa mu kaundula wa zipani mwezi uno usanathe ndipo chipanga mgwirizano ndi zipani zokhazo zimene zikuyika achimata patsogolo. Katswiri pa nkhani za ndale wonderful Mkhuche wati akukaika ngati chipanichi chikhale ndi nthawi yozigulitsila poti kwangotsala miyezi isanu ndi iwiri (7) kuti dziko lino lichititae chisankho mu mwezi wa Seputambala pa 16. Masiku apitawa guru lina linayambiysanso chipani china Cha National Youth Alliance ndipo akuti ndi cha achinyanata. (Daire Media Group)

INTRODUCING OUR FOURTH MEMBER

Meet John Barry Longwe, our Finance Controller at Daire Media Group.  With expertise in financial strategy and precision, He ensures our operations run smoothly and efficiently. His dedication to excellence drives the financial backbone of our success. We’re proud to have John Barry Longwe as part of our team
Mtsogoleri wachipani cha Democratic Proggresive Party (Dpp) Professor Ather Peter Muntharika akuchititsa misonkhano yoimayima mu mzinda wa Blantyre ndipo pano wafika kwachemusa. Mwazina Muntharika watsindika kuti ndiokonzeka kulamulanso dziko lino ngati anthu angazamupatse voti pa chisankho Chapa 16 September 2025. Muntharika akuti akazamusankha azathana ndi mavuto omwe anthu mdziko muno akukumana nawo pakadali pano. Mtsogoleriyu walimbikitsanso anthu kuti akalembetse mu kaundula wachibwerenza cha kalembela wa chisankho yemwe akuyambiranso posachedwapa. (Wolemba Alice Moyo)

INTRODUCING OUR THIRD MEMBER

We’re proud to introduce Desire Chirwa as the News Editor at Daire Media Group. With exceptional editorial skills and a passion for impactful journalism, she will lead our newsroom with dedication and vision.

MUM SEEKS RECONCILIATION WITH HER REBELLIOUS SONS AFTER YEARS IN HIDING FROM MURDER PLOT

A staged murder that forced mum to escape from her biological sons has finally come on the spotlight after the mother refreshes love and memories for her rebellious children after 19 years in hiding. Picture taken on X The mother whom we have named Mrs Kamanga for security reasons speaks out how she escaped and survived a murder plot by her two biological sons in company of their friends that led the family into a verge of dismantling the bond that existed between mother and children. No one knew the whereabouts of Mrs Kamanga until the day of this publication when this reporter bumped into the widow's merchandise after years of hiding in Mzimba when family relations bayed for her blood. She was accused of having a hand into the death of their husband and her daughter. The widow is now running a chain of business merchandise and feels it is time to re-connect and re-unite with her sons. Although she is still scared that her sons may still want her head but she believes that ev...

MALUBA ALBUM RELEASE

The Mzuzu based afro artist Merchah is set to release his first ever album titled "Maluba" on 30th January 2025 Before this new release the Afro Star whose real name is Uchizi Msowoya has produced other new songs which were released in 2024 in which he had featured among other renowned local artists Namadingo and Suffix.
Mtsogeleri wa Chipani Cha People's Development Kondwani Nankhumwa wauza khwimbi lomwe linasonkhana pa Sukulu ya Pulayimale ya Chindola m'boma la Mulanje kuti ndiyekhawo amene ali ndi kuthekera kodzathetsa mavuto akadzawavotera kukhala mtsogeleri wa dziko lino. Iwo anenetsa kuti dziko lino likukumana ndi mavuto womwe akufunika utsogoleri watsopano ponena kuti utsogoleri wotere uli mwa iwo. Asanapange chipani chawo a Nankhumwa anali wachiwiri kwa mtsogeleri wachipani chimene chinali m'boma Cha DPP ku chigawo chakumwera komanso anakhalapo nduna ya bomolo. Wolemba Alice Moyo

BWALO LA MILANDU LATULUTSA A SULEIMAN PA BELO

Bwalo la milandu ku Blantyre latulutsa pa belo a Sameer Suleiman womwe Polisi ya Blantyre inawamanga lolemba atakazipereka wokha. Asanamangidwe a Suleiman anamva kuti aPolisi akuwafuna pa Mulandu womwe malingana ndi aPolisi akuwaganizira kuti anafalitsa uthenga wabodza wokhudza anthu ena atatu. Malingana ndi aPolisi woganiziridwawa adanena pa msonkhano wina wandale kuti Dr Ken Zikhale Ng'oma, Richard Chinwendo Banda komanso Baba Steve Malondela amachita upo wofuna kuwapha. Lisanawatulutse bwalo la Blantyre magistrate linati a Suleiman akuyenera kupereka ndalama yokwana 500,000 kwacha komanso chikole Cha 2 million kwacha kuchokera kwa mboni ziwirizi. Iwo awalamulanso kuti apereke zitupa zawo zoyendera komanso azikawonekera ku likuru la Polisi ku chigawo chakumwera kamodzi pa mwezi. Olemba Phales Nthambo

SUSPENSION OF OPERATIONS AT NTCHEU PUMA SERVICE STATION

Ntcheu Puma Filling Station has its operational services been suspended for allegedly flouting procedures of selling fuels. The Malawi Energy Regulatory Authority (MERA) who has effected the suspension says selling fuels to customers in jerrycans and gallons is illegal. The suspension will be lifted subject to satisfactory implementation of measures taken to avoid reoccurrence of the malpractice, according to MERA. MERA said it will not hesitate to take necessary actions against service stations that violate measures stipulated by the regulator. The Authority has since urged consumers to report such malpractices. Daire Media Group

NEW GOVERNOR FOR RESERVE BANK OF MALAWI

Dr McDonald Mafuta Mwale has been appointed new Reserve Bank of Malawi (RBM) Governor replacing Dr William Banda who has since been fired in the recent cabinet re-configuration. This follows a press statement released by the state house and signed by its secretary, Coleen Zamba late Monday. According to the statement. Dr Mafuta Mwale will be Deputized by Dr Kisu Simwaka. The two appointments are subject to confirmation by Public Appointments Committee of the Malawi Parliament. By Alice Moyo

INTER-UNIVERSITY DIVINE SESSIONS TO UNLOCK DREAM INTERPRETATION

Online divine sessions have been singled out to help university students to unlock their Dream & Interpretations challenges. This will be hosted by the Inter-university Prayer Group and will be led by a renowned speaker Sir Joseph Nyirongo. The event which takes place this Friday from 7:30 PM via a WhatsApp chart group is expected bring solutions to those who struggle to interpret their dreams. As an expert in Biblical dream interpretation and spiritual teachings, Nyirongo will guide participants in exploring the spiritual and symbolic meanings of dreams. Attendees will gain valuable insights into decoding and applying dreams to daily life. This live session aims to attract students and believers seek wisdom on divine messages through dreams.  Questions and discussions will deepen the understanding of parterkers and then they will be asked to join and attend the WhatsApp groups. By Chrisy Zimba

INTRODUCING OUR SECOND MEMBER

Introducing to you, Busiso Kaunda, a valued team member at Daire Media Group! She specializes in News Reporting and is driven by creativity and collaboration.

APOLISI AMANGA A MWANAMVEKA NDI ENA ANAYI

Nduna yakale yazachuma Joseph Mwanamveka ayimanga pamodzi ndi anthu ena anayi powaganizira kuti akukhudziwa pa milanudu yokhuza katangale ku kampani ya Salima Sugar. Mneneri wa polisi mu dziko muno Peter Kalaya watsimikiza za nkhaniyi ponena kuti ena amene awamanga ndi mkulu wakale wa bungwe la Malawi Energy Regulatory Authority, (MERA) Collings Magalasi, mlembi wamkulu wakale ku office ya Pulezidenti Lloyd Muhara, mlembi ku nthambi yamsungichuma Cliff Chiunda ndi Jimmy Kusamale. Pakadali pano anthuwa awatengera ku Polisi yaku Area 6 ku Lilongwe kumene akuyembekezera kuwatengera ku khothi kuti akawatsegulire mulandu.  Wolemba Phales Nthambo

BULLETS HIRES MPONDA AS HEAD COACH.

FCB Nyasa Big Bullets has signed its former captain and assistant coach Peter Mponda who has resigned from Silver Strikers as head coach. Mponda takes over a three year contract from Casto Pasuwa who has been linked with reports that he may be joining the Malawi National team (The Flames). Chief Executive officer for the People's team Albert Chigoga has confirmed of unveileiling their man back on the People's board today. Peter Mponda became controvert when he resigned from the bankers soon after he earned the 2024 TNM Superleague championship and consequently signed an extended three year contract with the capital city giants. Before going to Silver Strikers Mponda had been coaching some team abroad. Silver Strikers executives were quoted in the country's dailies warning that any local club reported to have roped in Mponda will bare the repayment of a contract close of K26 million. It is not yet known whether Bullets or Mponda has paid back the said amount to Reserve Bank...

OUR FIRST MEMBER

Ladies and gentlemen, we’re thrilled to introduce to you, Taonga Jeka, a talented member of the Daire Media Group team! Taonga Jeka brings creativity, passion, and dedication to every project. She plays a key role in helping us deliver innovative solutions and drive impactful results.

TEAM INTRODUCTION AS WE PROGRESS IN 2025

Daire Media Group is delighted to start introducing its team as of today, 6th January 2025. Please be on the look out

NEW CABINET FOR PRESIDENT LAZARUS CHAKWERA

 President Lazarus Chakwera has reshuffled his cabinet effective 31st December 2024. In a press statement released today signed by the secretary to the president and cabinet Collen Zamba,some have been replaced by others. Jessy kabwira has been appointed as the minister of education,Monica Chayang'anamuno has replaced Harry Mkandawire as the minister of defence, Ezekiel Peter Ching'oma as the minister of homeland security replacing Kenneth Zikhale Ng'oma who has been appointed as the minister of mining. Most of the cabinet ministers have maintained their positions. Reported by Phales Nthambo