Namondwe wa Dikeledi amene wabuka lachinayi pa nyanja ya mchere ya India akuyembekezeka kufika mdziko la Mozambique la Mulungu lino.
Nthambi yowona za nyengo ku Malawi kuno ndi imene yanena izi mu uthenga wake wa lachinayi.
Nthambiyi yati pakadali pano palibe zizindikiro zoti Namondweyo atha kufika mdziko muno.
By Alice Moyo

Comments
Post a Comment